Fotokozani Bitcoin ngati ndili ndi zaka zisanu

Lolembedwa ndi Nik Custodio 2013/12/12open in new window

If you still canโ€™t figure out what the heck a bitcoin isโ€ฆ

Ngati simukudziwa kuti ndi chayani......

Takhalani pa bench .Ndi tsiku lopambanana.

Ndili ndi apple modzi ndi ine. Ndakupatsa.

Tsopano muli ndi apple modzi ime ndilibe kathu.

Izi ndi zophweka, sichoncho.

Tiyeni tione bwino zimene zinachitika:

Apple wanga anaikidwa mmanja mwanu.

Mukudziwa zimene zinachitika . Ndinaliko, munaliko , munagwila.

Sitinkafuna wachitatu pamenepo kuti atidzandize . sitimafunika kukoka malume tommy (omwe ndi oweruza otchuka) kuti akhale nafe pa benchi ndikutsimikizira kuti apple anachoka kwa ine ndikupita kwa inu

Apple ndi yanu! Sindingakupatseni apple wina chifukwa ndilibe zotsalira sindingathe kuzilamulira . apple inandisiya yathunthu. Muli ndi ulamuliro wonse pa Apple uja tsopano. Mutha kumupatsa nzanu ngati mukufuna , kenako mnzanuyo akhoza kuperekanso kwa mnzake. Ndi zina zotero.

Kotero ndi momwe kusithana kwa-muthu kumawonekera. Ndikuganiza ndi zofanana kaya ndi kukupatsani nthochi , buku , kapena kunena kotala , kapena ndalama ya dollar......

Koma ndikuziyang'anira ndekha.

Tabwerela ku ma applezi

Tsopano nenani , ndili ndi apple limodzi la digital . pano ndikupatsani apple yanga ya digital

Ah! Pano zikuma sangalatsa

Mukudziwa bwanji kuti apple la digital lomwe kale linali langa, Tsopano ndi lanu , ndipo ndilanu lokha ? Ganizirani izi kachiwiri

Ndizovuta kwambiri , si choncho? Mukudziwa bwanji kuti sindinatumize apple wina kwa malume tommy ngati cholumikizira email poyamba? Kapena nzako joe? Kapena mzanga Lisa nayeso?

Mwina mwake ndina panga makope angapo a apple la digital pa computer yanga . mwina ndina ika pa internet ndipo athu million anaona

Monga mukuonera, kusithana kwa digital ndi mavuto pang'ono . kutumiza ma apple a digital sikuoneka ngati kutumiza ma apple eni eni

A science ena anzeru pa computer ali ndi dzina la vutoli: liamatchedwa vuto lowonongera kawiri. Koma musadandaule za izi zomwe muyenera kudziwa ndikuti zosokonezeka iwo kwa thawi thawi yayitali ndipo sanazithese. Mpaka pano.

Koma tiyeni tiyese kulingalila yanko patokha.

Ostogolera

Mwina mwake ma apple a digital amafunika kuwatsata m'buku ndi buku lomwe mumayang'ana zochitika zonse-buku lowerengera ndalama

Buku ili popeza ndi digital liyenera ndi wina wowayanga'nira

Nenanu monga dziko la Warcraft . blizzard. Anyamata omwe adapanga masewerawa pa internet, ali ndi "buku la digital" la malupanga a moto osowa omwe amapezeka m'dongosolo lawo . chifukwa chake wina ngati iwo amatha kudziwa ma apple athu a digital . zodabwitsa! - tinazithetsa

Mavuto

Pali vuto pango'ono ngakhale:

  1. Nanga bwanji ngati muthu wina waku Blizzard adapanga zambiri? Amatha kungo onjezera ma digital angapo: ma apple kuri azikhala bwino thawi iliyonse yomwe angafune!

  2. Sizofanana ndendende pomwe tidali pa bench tsiku limodzi. Tinali inu ndi ine basi ndiye. Kudutsa blizzard kuli ngati kukoka malume tommy (kachitatu) kunja kwa khothi ( kodi ndinanena kuti ndi oweruza otchuka?) Pazogulitsa zathu zose pa bench ya paki. Kodi ndingangopereka apple yanga ya digital kwa inu, monga mukudziwa, mwanjira ya thawi zonse

Kodi pali njira iliyonse yotengera bench yathu ku paki, kungoti inu ndi ine zomwe timachita za digital .zikuoneka ngati zovuta...

Njira yothesera

Bwanji ngati titapereka bukhu ili-kwa aliyese m'malo mokhala m'ma computer pa blizzard , izikhala m'ma computer a aliyense . zochitika zonse zomwe zidachitikapo kuyambira thawi zonse m'ma apple a digie zidzajambulidwamo

Simungathe kubera. sindingaku tumizileni ma apple a digital omwe ndilibe , chifukwa ndiye kuti samalumikizana ndi aliyese m'dongosolo. Kunga khale kovuta kuti mu menye. Maka maka ngati yayamba kukula.

Kuphatikiza apo samayanga'niridwa ndi muthu m'modzi chifukwa ndikudziwa kuti palibe amene angangodziperekela ma apple ena a digital. Malamulo a dongosololi anali atatchulidwa kale koyambirira. Ndipo malamulo ndi malamulo ndi otseguka. Alipo athu anzeru ena atithandizira mu chitetezo , kusitha ,ndikuwaunikiranso athu

Mutha kutenga nawo mbali yapa network iyi ndikusithaso zolembazo ndikuwonetsetsa kuti zonse zatuluka . pazovuta muthaka kukala ndi ma apple a digital 25 ngati mphoto , ndipo ndi njira yomweyo yopangira ma apple a digital ambiri

Ndinachepetsa pango'no

โ€ฆ Koma njira imene ndinafotokozayo ilipo. Imatchedwa kuti bitcoin protocol . ma apple a digital aja nde "bitcoins " mkati mwa dongosolo. Zosangalatsa !

Kotero. Kodi mwaona zomwe zinachitika? Kodi zolembera pagulu zimathandizila chiyani?

  1. Ndi gwero otseguka mukumbukira? Chiwerengero chonse chama apple chimafotokozedwa pagulu mu bukhu kumayambiriro. Ndikudziwa kuchuluka komwe kulipo.mutjawi imeneyi ndikudziwa kuti ndiochepa (osowa).

  2. Ndikasitha ndikudziwa kuti apple wa digital siwangaso pano ndiwanu. Sindinkatha kunena izi pa zithu za digital. idzasithidwa ndikutsimikiziridwa ndi buku lolembera

  3. Popeza ndi buku lowerengera athu. Sikufunika malume tommy(wachitatu) kuti atsimikizire kuti ine sindinabele, kaoena kuzipangira ndekha kapena kutumiza ma apple kawiri kapena katatu

    Muthawi imeneyi ,kusinthana kwa apple wa digital pano kulingati kusithana apple wa pa manja.tsopano zilingati kuona apple akuchoka manja mwanga ndikugwa mu nthumba mwanu . ndipo ngati pa bench pa ku paki tinalipo athu awiri malume tommy masafunika kuti atsimikizere.

Mwanjira ina imakhala yapathupi

Mukudziwa zomwe zilli zabwino? Zinakali digital. Tsopano thitha kuthana ndi ma apple 1,000 kapena 1 million apples kapena 0000001apples Nditha kutumiza podina batani ndipo ndithaso kuku ikirani mu thumba lanu ya digital olo muthakhala ku dziko lina ine ndili new York ndikoza kutumizaba.

Nditha kupanga zithu zina za digital kukwera pa mwamba pa ma apple a digital wa poti nazoso ndi digital mwinaso nditha kulumikiza mawu. Ndithaso ku lumikiza zithu zofunika ngati nambala, kapena stock certificate ,kapena chiphaso...

Kotero izi ndizabwino! Kodi ti gwiritsa ntchito bwanji ma apple a digital wa ndizothandiza kwambiri eti?

Athu ambiri akutsutsana za izi . tsopano pali kutsutsana pakati pa izi ndi sukulu ya chuma pakati pa andale. Pakati pa opanga mapulogramu. Osamvera athu osewa.ngakhale athu ena ndi a nzeru. Ena amanamizidwa. Ena amati dongosololi lilofunika kwa mbiri. Ena amati sizofunika

Nyamata wina anayika nambala yovuta:$ 1,300 pa apple. ena mati ndi golide wa digital, ena ndalama, ena amati alingati tulips, ena amati zisitha dziko lapansi, ena amati ndi chi zolowezi chabe

Ndili ndi maganizo anga pa izi.

Imeneyo ndi nkhani ya nthawi ina. Koma mwana, tsopano mukudziwa zambiri za Bitcoin kuposa ambiri.

Recommend Reading (Updated 2017)

โ€œYou Donโ€™t Understand Bitcoin Because You Think Money is Realโ€open in new window by Maria Bustillosopen in new window is a good follow-up read.

You can also read more about Ethereum and Smart Contracts hereopen in new window. Enjoy!

Omasulira
I-star Magagula

Othandizira
BitMEX