Bitcoin ili ngati masewera

by @thebitcoinrabbi 2021/01/13open in new window

Thawi zambiri ndakhala ndikulongosola momwe #bitcoin imagwirira ntchito ndipo imakhazikika pantchito yamasewera. Ndikuona kuti zimathandiza kuyakha mafuso a wamba.:

Q: Ndani anayambitsa basketball?
A: Palibe amene akudziwa. Koma aliyese pa dziko lapansi akhoza ku sewera. Zilibe kathu kuti wopangayo alufuna kusitha malamulo kapena kuzi patsa ma points kapena china chilichonse. Sitisamala zomwe amaganiza pamasewera athu.

Q: ndani akuyang'anira ma sewerawa?
A: palibe amene akuyang'anira, tonse tinangoganiza zosewera. Tonse timadziwa. Ndikutsatila malamulo. Ndipo ngati wina wabera, amachotsedwa pamasewera ngati wina wapeza ma points ambiri sitimadanda ula

Q: tiziwa bwanji kuti malamulo sasitha?
A: tonse tidavomereza nawo pomwe timayamba kusewera ndipo aliyese amene akufuna kusewera ndi malamulowa atha kusewera, ndipo ngati wina akufuna kusintha afunika ku sewera kwina.

Q: kodi sizingabedwe?
A: chilichonse chimaomekera poyera. Tomse thitha kuona gawo lonse ndi zambiri zonse ngati wina amabela, tomse tinakadziwa ndikuwauza kuti atuluke.

Q: chifukwa chiyani ili ndi phindu lililonse?
A: tonse tinasanka kusewera chifukwa ndiyofunika kwa ife.ngati wina akufuna kulowa nawo, tiyenera kuvomeleza mfundo zathu ndi kufunika kwake

Ndimayi yamikira .kotero ili ndi phindu mtengo ndiwo khazikika

Q: kodi sizinga letsedwe?
A: mwina koma pali athu ena we amatha kusewera ndi ndodo ndi mpira osa pweteka wina aliyese mwina boma itha kukuletsani kusewera koma sangathe kuletsa lingalilo lomenya mpira ndi ndido masewera atha kupitilila kwina kwake.

Q: ndiyenera kujoyina?
A: pangazi zomwe mukufuna, ndimasewra baseball, mutha kulowa nawo kapena mutha kulowa HFPS.

Omasulira
I-star Magagula

Othandizira
BitMEX