Takulandilani ku Bitcoin, obwera kumene!

by Jameson Lopp 2017/11/19open in new window

Mafuso ofusidwa kawiri kawiri:

Q: Ndiyenera ku khulipira ndani?
A: Palibe.

Q: Ndiyenera ku gulitsa liti?
A: Palibe.

Q: Kodi bitcoin ikufa chifukwa ____?
A: ayi.

Q: Kodi ndazilowetsa mu chani?
A: Palibe amene akudziwa.

Q: Ndiphuzira bwanji za mbiri?
A: Tili ndi chuma cha mbiri pano. Kapena mutha ku pita ku lopp.netopen in new window

Omasulira
I-star Magagula

Othandizira
BitMEX