Ndine wolemba

by GameKyuubi 2013/12/18open in new window

Ndinalemba mutuwo kawiri chifukwa ndimadziwa kuti sizolondola thawi yoyamba. komabe zolakwila. Mulimonse.

GF watuluka mu bar ya chinyamata Mtengo wa bitcoin ukuwonongeka. Chifukwa chani ndiku gwilitsa . ndikuuzani chifukwa chani

Ndi chifukwa choti ndine wopanga malonda oyipa ndipo ndikudziwa kuti ndimachita zithu zoipa. Eya inu amalonda abwino mutha kuona zokwera komanso zotsika pansi pat piffy wing wong wang monga choncho ndikupanga million

ndalama ndithu palibe vuto bro.

Chimodzimodzinso manja ofooka amakhala ngati OH AYI AKUPITA NDIDZAGULITSA he he ndiye amakhala ngati OH GOD MY ASSHOLE pomwe amalonda a SMART omwe AMADZIWA ZOMWE AKUCHITA amagulanso koma mukudziwa chiyani? Ine sindine wa gulu limenelo. Pamene amalonda amagulanso ine ndimakhala kale gawo la likulu la msika kotero GANIZANI NDANI MUKUNYENGA amalonda amasiku OSATI INE-!

Ulusi wamwano uja umati "OHH MUKAGWIRITSA NTCHITO" EYA NO SHIT. NO SHIT!

ANAYENERA KUGULITSA. NDIKAFUNA KUGULITSA KANTHAWI ALIYENSE NDISAMAGULITSA NDI

UNAGULA KANTHAWI ALIYENSE ALIYENSE KOMA MUMADZIWA ZOTI SI ALIYENSE

NDI WABWINO NGATI INU.

Mukungogulitsa pamsika wa zimbalangondo ngati ndinu wogulitsa tsiku labwino kapena noob wonyenga. Anthu apakati agwira.

Mu masewera a zero-sum monga awa, amalonda amatha kutenga ndalama zanu ngati mutagulitsa.

Omasulira
I-star Magagula

Othandizira
BitMEX